6 Ndipo tinapita m'ngalawa kucokera ku Filipi, atapita masiku a mkate wopanda cotupitsa, ndipo popita masiku asanu tinawapeza ku Trowa; pamenepo tinatsotsa masiku asanu ndi awiri.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20
Onani Macitidwe 20:6 nkhani