Macitidwe 21:13 BL92

13 Pamenepo Paulo anayankha, Mucitanji, polira ndi kundiswera mtima? pakuti ndakonzeka Ine si kumangidwa kokha, komatunso kufera ku Yerusalemu cifukwa ca dzina la Ambuye Yesu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21

Onani Macitidwe 21:13 nkhani