Macitidwe 21:18 BL92

18 Ndipo m'mawa mwace Paulo analowa nafe kwa Yakobo; ndi akulu onse anali pomwepo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21

Onani Macitidwe 21:18 nkhani