18 ndipo ndinamuona iye, nanena nane, Fulumira, turuka msanga m'Yerusalemu; popeza sadzalandira umboni wako wakunena za Ine.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22
Onani Macitidwe 22:18 nkhani