20 ndipo pamene anakhetsa mwazi wa Stefano mboni yanu, ine ndemwe ndinalikuimirirako, ndi kubvomerezana nao, ndi kusunga Zoobvala za iwo amene anamupha iye.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22
Onani Macitidwe 22:20 nkhani