17 Ndipo Paulo anadziitanira kenturiyo wina, nati, Pita naye mnyamata uyu kwa kapitao wamkuru; pakuti ali nako kanthu kakumfotokozera iye.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23
Onani Macitidwe 23:17 nkhani