Macitidwe 23:27 BL92

27 Munthu uyu anagwiridwa ndi Ayuda, ndipo akadaphedwa ndi iwo; pamenepo ndinafikako ine ndi asilikari, ndipo ndinamlanditsa pakumva kuti ndiye Mroma.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:27 nkhani