Macitidwe 23:29 BL92

29 Ndipo ndinapeza kuti adamnenera za mafunso a cilamulo cao; koma analibe kumnenera kanthu kakuyenera imfa kapena nsinga.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:29 nkhani