Macitidwe 24:14 BL92

14 Koma ici ndibvomera kwa inu, kuti monga mwa Njira yonenedwa mpatuko, momwemo nditumikira Mulungu wa makolo athu, ndi kukhulupira zonse ziri monga mwa cilamulo, ndi zolembedwa mwa aneneri;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 24

Onani Macitidwe 24:14 nkhani