Macitidwe 24:27 BL92

27 Koma zitapita zaka ziwiri Porkiyo Festo analowa m'malo a Felike; ndipo Felike pofuna kukonda Ayuda anamsiya Paulo m'nsinga.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 24

Onani Macitidwe 24:27 nkhani