5 Pakuti tapeza munthuyu ali ngati mliri, ndi woutsa mapanduko kwa Ayuda onse m'dziko lonse lokhalamo anthu, ndi mtsogoleri wa mpanduko wa Anazarene;
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 24
Onani Macitidwe 24:5 nkhani