Macitidwe 25:20 BL92

20 Ndipo ine posinkhasinkha za mafunso awa ndinamfunsa ngati afuna kupita ku Yerusalemu, ndi kuweruzidwa komweko za izi.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 25

Onani Macitidwe 25:20 nkhani