Macitidwe 26:16 BL92

16 Komatu uka, imirira pa mapazi ako; pakuti cifukwa ca ici ndinaonekera kwa iwe, kukuika iwe ukhale mtumiki ndi mboni ya izi wandionamo Ine, ndiponso ya izi ndidzakuonekeramo we;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 26

Onani Macitidwe 26:16 nkhani