Macitidwe 26:20 BL92

20 komatu kuyambira kwa iwo a m'Damasiko, ndi a m'Yerusalemu, ndi m'dziko lonse la Yudeya, ndi kwa amitundunso ndinalalikira kuti alape, natembenukire kwa Mulungu, ndi kucita nchito zoyenera kutembenuka mtima.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 26

Onani Macitidwe 26:20 nkhani