Macitidwe 26:22 BL92

22 Pamenepo pothandizidwa ndi Mulungu, ndiimirira kufikira lero lino, ndi kuwacitira umboni ang'ono ndi akuru, posanena kanthu kena koma zimene aneneri ndi Mose ananenazidzafika;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 26

Onani Macitidwe 26:22 nkhani