Macitidwe 26:29 BL92

29 Ndipo Paulo anati, Mwenzi atalola Mulungu, kuti ndi kukopa pang'ono, kapena ndi kukopa kwambiri, si inu nokha, komatunso onse akundimva ine lero, akadakhala otero onga ndiri ine, osanena nsinga izi.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 26

Onani Macitidwe 26:29 nkhani