Macitidwe 27:10 BL92

10 nanena nao, Amuna inu, ndiona ine kuti ulendo udzatitengera kuonongeka ndi kutayika kwambiri, si kwa akatundu okha kapena ngalawa yokha, komatunso kwa moyo wathu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 27

Onani Macitidwe 27:10 nkhani