17 ndipo m'mene adaukweza, anacita nazo zothandizira, nakulunga ngalawa; ndipo pakuopa kuti angatayike pa Surti, anatsitsa matanga, natengedwa motero.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 27
Onani Macitidwe 27:17 nkhani