Macitidwe 27:21 BL92

21 Ndipo pamene atakhala nthawi yaikuru osadya kanthu, Paulo anaimirira pakati pao, nati, Amuna inu, mukadamvera ine, osacoka ku Krete, osadzitengera kuonongeka ndi kutayika kumene.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 27

Onani Macitidwe 27:21 nkhani