Macitidwe 27:27 BL92

27 Koma pofika usiku wakhumi ndi cinai, potengedwa ife kwina ndi kwina m'nyanja ya Adriya, pakati pa usiku amarinyero anazindikira kuti analikuyandikira kumtunda;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 27

Onani Macitidwe 27:27 nkhani