Macitidwe 27:3 BL92

3 Ndipo m'mawa mwace tinangokoceza ku Sidoni; ndipo Yuliyo anacitira Paulo mwacikondi, namlola apite kwa abwenzi ace amcereze.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 27

Onani Macitidwe 27:3 nkhani