Macitidwe 28:21 BL92

21 Ndipo anati kwa iye, Ife sitinalandira akalata onena za inu ocokera ku Yudeya, kapena sanadza kuno wina wa abale ndi kutiuza kapena kulankhula kanthu koipa ka inu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 28

Onani Macitidwe 28:21 nkhani