27 Pakuti mtima wa anthu awa watupatu,Ndipo m'makutu mwao mmolemakumva,Ndipo masoao anawatseka;Kuti angaone ndi maso,Nangamve ndi makutu,Nangazindikire ndi mtima,Nangatembenuke,Ndipo Ine ndingawaciritse.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 28
Onani Macitidwe 28:27 nkhani