Macitidwe 28:4 BL92

4 Koma pamene akunjawo anaona ciromboco ciri lende pa dzanja lace, ananena wina ndi mnzace, Zoona munthuyu ndiye wambanda, angakhale anapulumuka m'nyanja, cilungamo sicimlola akhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 28

Onani Macitidwe 28:4 nkhani