7 Koma pafupt pamenepo panali minda, mwini wace ndiye mkulu cisumbuco, dzina lace Popliyo; amene anatilandira ife, naticereza okoma masiku atatu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 28
Onani Macitidwe 28:7 nkhani