Macitidwe 4:13 BL92

13 Koma pakuona kulimbika mtima kwa Petro ndi Yohane, ndipo pozindikira kuti ndiwo anthu osaphunzira ndi opulukira, anazizwa ndipo anawazindikira, kuti adakhala pamodzi ndi Yesu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:13 nkhani