Macitidwe 4:21 BL92

21 Koma m'mene anawaopsanso anawamasula, osapeza kanthu kakuwalanga, cifukwa ca anthu; pakuti onse analemekeza Mulungu cifukwa ca comwe cidacitika.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:21 nkhani