Macitidwe 4:24 BL92

24 Ndipo m'mene adamva, anakweza mau kwa Mulungu ndi mtima umodzi, nati, Mfumu, Inu ndinu wolenga thambo la kumwamba ndi dziko, ndi nyanja, ndi zonse ziri m'menemo;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:24 nkhani