10 Ndipo anagwa pansi pomwepo pa mapazi ace, namwalira; ndipo analowa anyamatawo, nampeza iye wafa, ndipo anamnyamula kuturuka naye, namuika kwa mwamuna wace.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 5
Onani Macitidwe 5:10 nkhani