25 Ndipo anadza wina nawafotokozera, kuti, Taonani, amuna aja mudawaika m'ndende ali m'Kacisi, alikuimirira ndi kuphunzitsa anthu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 5
Onani Macitidwe 5:25 nkhani