37 Atapita ameneyo, anauka Yuda wa ku Galileya, masiku a kulembedwa, nakopa anthu amtsate. Iyeyunso anaonongeka, ndi onse amene anamvera iye anabalalitsidwa.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 5
Onani Macitidwe 5:37 nkhani