39 koma ngati icokera kwa Mulungu simungathe kuwapasula; kuti kapena mungapezeke otsutsana ndi Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 5
Onani Macitidwe 5:39 nkhani