16 ndipo anawanyamula kupita nao ku Sukemu, nawaika m'manda amene Abrahamu adagula ndi mtengo wace wa ndalama kwa ana a Emori m'Sukemu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:16 nkhani