23 Koma pamene zaka zace zinafikira ngati makumi anai, kunalowa mumtima mwace kuzonda abale ace ana a Israyeli,
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:23 nkhani