25 Ndipo anayesa kuti abale ace akazindikira kuti Mulungu alikuwapatsa cipulumutso mwa dzanja lace; koma sanazindikira.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:25 nkhani