32 5 akuti, Ine ndine Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abrahamu, ndi wa Isake, ndi wa Yakobo. Ndipo Mose ananthunthumira, osalimbika mtima kupenyetsako.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:32 nkhani