45 17 Cimenenso makolo athu akudza m'mbuyo, analowa naco ndi Y oswa polandira iwo zao za amitundu, 18 amene Mulungu anawaingitsa pamaso pa makolo athu, kufikira masiku a Davine;
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:45 nkhani