Macitidwe 7:49 BL92

49 21 Thambo la kumwamba ndilo mpando wacifumu wanga,Ndi dziko lapansi copondapo mapazi anga:Mudzandimangira nyumba yotani? ati Ambuye;Kapena malo a mpumulo wanga ndi otani?

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7

Onani Macitidwe 7:49 nkhani