58 ndipo 27 anamtaya kunja kwa mudzi, namponya miyala; ndipo 28 mbonizo zinaika zobvala zao pa mapazi a mnyamata dzina lace Saulo.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:58 nkhani