Macitidwe 8:1 BL92

1 Ndipo Saulo analikubvomerezana nao pa imfa yace. Ndipo tsikulo kunayamba kuzunza kwakukuru pa Mpingo unali m'Yerusalemu; ndipo anabalalitsidwa onse m'maiko a Yudeya ndi samariya, koma osati atumwi ai.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 8

Onani Macitidwe 8:1 nkhani