Macitidwe 9:19 BL92

19 ndipo ananyamuka nabatizidwa; ndipo analandira cakudya, naona naco mphamvu.Ndipo anakhala pamodzi ndi akuphunzira a ku Damasiko masiku ena.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:19 nkhani