34 Ndipo Petro anati kwa iye, Eneya, Yesu Kristu akuciritsa iwe; uka, yalula mphasa yako. Ndipo anauka pomwepo.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9
Onani Macitidwe 9:34 nkhani