Macitidwe 9:36 BL92

36 Koma m'Yopa munali wophunzira dzina lace Tabita, ndilo kunena Dorika; mkazi ameneyo anadzala ndi nchito zabwino ndi zacifundo zimene anazicita.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:36 nkhani