2 Ndipo Davide anati kwa Yoabu ndi kwa akuru a anthu, Kawerengeni Israyeli kuyambira ku Beereseba kufikira ku Dani; nimundibwezere mau, kuti ndidziwe ciwerengo cao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21
Onani 1 Mbiri 21:2 nkhani