1 Mbiri 29:6 BL92

6 Pamenepo akuru a nyumba za makolo, ndi akuru a mafuko a Israyeli, ndi akuru a zikwi ndi a mazana pamodzi ndi iwo oyang'anira nchito ya mfumu, anapereka mwaufulu,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:6 nkhani