1 Mbiri 29:7 BL92

7 napereka ku utumiki wa nyumba ya Mulungu golidi matalente zikwi zisanu, ndi madariki zikwi khumi; ndi siliva matalente zikwi khumi, ndi mkuwa matalente zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu, ndi citsulo matalente zikwi zana limodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:7 nkhani