1 Mbiri 29:8 BL92

8 Ndipo amene anali nayo miyala ya mtengo wace anaipereka ku cuma ca nyumba ya Yehova, mwa dzanja la Yehieli Mgerisoni.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:8 nkhani