1 Mbiri 29:9 BL92

9 Ndipo anthu anakondwera popeza anapereka mwaufulu; pakuti ndi mtima wangwiro anapereka mwaufulu kwa Yehova; mfumu Davide yemwe anakondwera ndi cimwemwe cacikuru.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:9 nkhani