Yobu 1:4 BL92

4 Ndipo ana ace amuna anamuka kukacita madyerero m'nyumba ya yense pa tsiku lace; natumiza mthenga kuitana alongo ao atatu adzadye nadzamwe nao.

Werengani mutu wathunthu Yobu 1

Onani Yobu 1:4 nkhani