Macitidwe 1:11 BL92

11 amenenso anati, Amuna a ku Galileya, muimiranji ndi kuyang'ana kumwamba? Yesu amene walandiridwa kunka Kumwamba kucokera kwa inu, adzadza momwemo monga munamuona alinkupita Kumwamba.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 1

Onani Macitidwe 1:11 nkhani